Friday, June 19, 2009

conversation with my friend

Chifundo Tenthani M.: yea
ucizibi: My friend
Chifundo Tenthani M.: wasup my friend?
ucizibi: Writing the final paper my friend. And U? Ukumwa?
Chifundo Tenthani M.: i have beer here but am not drinking now
ucizibi: OK. My friend ukufuna udziwe mmene ndikukhozera?
Chifundo Tenthani M.: tandiuze my friend
ucizibi: B+, A,B,A,B+,B+,A,A,B+,A,A kwatsala maResults awiri
Chifundo Tenthani M.: shashasha
Chifundo Tenthani M.: akupatsani nazo phd zimenezotu
ucizibi: Koma dinc ndamuphonya chifukwa cha B ayise
ucizibi: Aaaaah ndakayika
Chifundo Tenthani M.: ahhh modziyo eti?
ucizibi: Watsitsa grade ndithu ameneyo. Unless andipatse ma A+ in the remaining assignments
Chifundo Tenthani M.: ah ok amangotenga average regardless of some marks less than a certain mark?
ucizibi: B is above the threshold for awarding dinc anyway koma I doubt ngati average ingafike above A amane ali dincyo
ucizibi: Uyamba nthawi zanji kumwa?
Chifundo Tenthani M.: ah mwina sindimwa lero ndili mmudi yoipa kwabasi
ucizibi: Bwanji? Akukukaniza zijazi?
Chifundo Tenthani M.: hahaha
Chifundo Tenthani M.: nonono
Chifundo Tenthani M.: komano nthawi zina ndimatero
Chifundo Tenthani M.: i didnt even go out of this ka house
ucizibi: Aliyense amakhala ndinthawi yoteroyo. Even me
Chifundo Tenthani M.: eeetu nde ine lafika lero koma ndikaumwa mawa kuyambila mmamawa
ucizibi: Hahahaha. Ndiye kuti ukudziwa chimene chakubowa my friend.
Chifundo Tenthani M.: kenako ndikaonela game ya ma darts

No comments:

AddThis

Bookmark and Share